1 Mafumu 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Atayangʼana, anaona kuti kumutu kwake kuli mkate wozungulira pamiyala yotentha komanso jagi* ya madzi. Eliya anadya nʼkumwa ndipo anagonanso. 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:6 Tsanzirani, tsa. 103 Nsanja ya Olonda,7/1/2011, tsa. 20
6 Atayangʼana, anaona kuti kumutu kwake kuli mkate wozungulira pamiyala yotentha komanso jagi* ya madzi. Eliya anadya nʼkumwa ndipo anagonanso.