1 Mafumu 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atafika kumeneko, analowa mʼphanga+ nʼkugona mmenemo usiku wonse. Kenako anamva mawu a Yehova akufunsa kuti: “Ukudzatani kuno Eliya?” 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:9 Tsanzirani, tsa. 104 Nsanja ya Olonda,7/1/2011, tsa. 21
9 Atafika kumeneko, analowa mʼphanga+ nʼkugona mmenemo usiku wonse. Kenako anamva mawu a Yehova akufunsa kuti: “Ukudzatani kuno Eliya?”