-
1 Mafumu 19:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Koma Mulungu anati: “Tuluka, kaime paphiri pamaso pa Yehova.” Kenako Yehova anadutsa,+ ndipo kunawomba chimphepo champhamvu chomwe chinkangʼamba mapiri ndi kuphwanya matanthwe pamaso pa Yehova+ koma Yehova sanali mumphepoyo. Mphepoyo itatha kunachita chivomerezi,+ koma Yehova sanali mʼchivomerezicho.
-