1 Mafumu 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako Yehova anamuuza kuti: “Bwerera ndipo upite kuchipululu cha Damasiko. Ukakafika ukadzoze Hazaeli+ kuti akhale mfumu ya Siriya. 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:15 Tsanzirani, ptsa. 106-107 Nsanja ya Olonda,7/1/2011, tsa. 225/15/1997, tsa. 13
15 Kenako Yehova anamuuza kuti: “Bwerera ndipo upite kuchipululu cha Damasiko. Ukakafika ukadzoze Hazaeli+ kuti akhale mfumu ya Siriya.