1 Mafumu 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ukadzozenso Yehu+ mdzukulu wa Nimusi kuti akhale mfumu ya Isiraeli ndipo Elisa,* mwana wa Safati wa ku Abele-mehola, ukamudzoze kuti adzakhale mneneri mʼmalo mwako.+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:16 Nsanja ya Olonda,5/15/1997, tsa. 13
16 Ukadzozenso Yehu+ mdzukulu wa Nimusi kuti akhale mfumu ya Isiraeli ndipo Elisa,* mwana wa Safati wa ku Abele-mehola, ukamudzoze kuti adzakhale mneneri mʼmalo mwako.+