-
1 Mafumu 19:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Zitatero, Elisa anasiya ngʼombe zamphongozo nʼkuthamangira Eliya ndipo anamuuza kuti: “Ndiloleni ndipite ndikakise kaye bambo anga ndi mayi anga, kenako ndidzakutsatirani.” Eliya anamuyankha kuti: “Pita, sindingakuletse.”
-