1 Mafumu 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho anabwerera nʼkutenga ngʼombe zamphongo ziwiri zija nʼkuzipha.* Anatenga mitengo ya pulawoyo nʼkuphikira nyama ya ngʼombezo. Kenako anapatsa anthu kuti adye. Atatero, iye ananyamuka nʼkutsatira Eliya ndipo anayamba kumʼtumikira.+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:21 Nsanja ya Olonda,11/1/1997, ptsa. 30-31
21 Choncho anabwerera nʼkutenga ngʼombe zamphongo ziwiri zija nʼkuzipha.* Anatenga mitengo ya pulawoyo nʼkuphikira nyama ya ngʼombezo. Kenako anapatsa anthu kuti adye. Atatero, iye ananyamuka nʼkutsatira Eliya ndipo anayamba kumʼtumikira.+