1 Mafumu 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Beni-hadadi+ mfumu ya Siriya+ anasonkhanitsa asilikali ake onse. Atatero ananyamuka pamodzi ndi mafumu ena 32 ndi mahatchi komanso magaleta awo ndipo anapita kukazungulira mzinda+ wa Samariya+ nʼkuyamba kumenyana nawo.
20 Beni-hadadi+ mfumu ya Siriya+ anasonkhanitsa asilikali ake onse. Atatero ananyamuka pamodzi ndi mafumu ena 32 ndi mahatchi komanso magaleta awo ndipo anapita kukazungulira mzinda+ wa Samariya+ nʼkuyamba kumenyana nawo.