-
1 Mafumu 20:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Choncho Ahabu anauza anthu amene anatumidwa ndi Beni-hadadi aja kuti: “Mukauze mbuyanga mfumu kuti, ‘Zonse zimene munandiuza poyamba, ine mtumiki wanu ndichita. Koma zimene mwanena kachiwirizi, sindingachite.’” Zitatero, anthuwo ananyamuka nʼkukapereka uthengawo kwa mfumu yawo.
-