-
1 Mafumu 20:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ndiyeno Beni-hadadi anatumizira Ahabu uthenga wakuti: “Milungu yanga indilange mowirikiza, ngati fumbi la ku Samariya lidzakwanire kuti anthu onse onditsatira apatsidwe lodzaza mʼmanja.”
-