1 Mafumu 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mfumu ya Isiraeli inayankha kuti: “Mukamuuze kuti, ‘Musayambe kudzitama nkhondo isanayambe ngati kuti mwapambana kale nkhondoyo.’”+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:11 Nsanja ya Olonda,7/1/2005, tsa. 31
11 Mfumu ya Isiraeli inayankha kuti: “Mukamuuze kuti, ‘Musayambe kudzitama nkhondo isanayambe ngati kuti mwapambana kale nkhondoyo.’”+