1 Mafumu 20:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Asilikali otsalawo anathawira mumzinda wa Afeki+ ndipo khoma linagwera 27,000 mwa asilikali amenewa. Nayenso Beni-hadadi anathawa nʼkukafika mumzindawo ndipo anakabisala mʼchipinda chamkati.
30 Asilikali otsalawo anathawira mumzinda wa Afeki+ ndipo khoma linagwera 27,000 mwa asilikali amenewa. Nayenso Beni-hadadi anathawa nʼkukafika mumzindawo ndipo anakabisala mʼchipinda chamkati.