1 Mafumu 20:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiyeno atumiki ake anamuuza kuti: “Tamva kuti mafumu a nyumba ya Isiraeli amakhala achifundo.* Tiyeni tivale ziguduli mʼchiuno nʼkumanga zingwe kumutu ndipo tipite kwa mfumu ya Isiraeli. Mwina sikakuphani.”+
31 Ndiyeno atumiki ake anamuuza kuti: “Tamva kuti mafumu a nyumba ya Isiraeli amakhala achifundo.* Tiyeni tivale ziguduli mʼchiuno nʼkumanga zingwe kumutu ndipo tipite kwa mfumu ya Isiraeli. Mwina sikakuphani.”+