1 Mafumu 20:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Mneneriyo anauza mfumuyo kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Chifukwa sunaphe munthu amene ndinanena kuti ayenera kuphedwa,+ moyo wako ulowa mʼmalo mwa moyo wake+ ndipo anthu ako alowa mʼmalo mwa anthu ake.’”+
42 Mneneriyo anauza mfumuyo kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Chifukwa sunaphe munthu amene ndinanena kuti ayenera kuphedwa,+ moyo wako ulowa mʼmalo mwa moyo wake+ ndipo anthu ako alowa mʼmalo mwa anthu ake.’”+