1 Mafumu 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako panachitika nkhani yokhudza munda wa mpesa wa Naboti wa ku Yezereeli. Mundawu unali ku Yezereeli,+ pafupi ndi nyumba yachifumu ya Ahabu mfumu ya Samariya.
21 Kenako panachitika nkhani yokhudza munda wa mpesa wa Naboti wa ku Yezereeli. Mundawu unali ku Yezereeli,+ pafupi ndi nyumba yachifumu ya Ahabu mfumu ya Samariya.