-
1 Mafumu 21:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Choncho Ahabu analowa mʼnyumba mwake ali wachisoni ndiponso wokhumudwa chifukwa cha zimene Naboti wa ku Yezereeli anamuuza kuti: “Sindikupatsani cholowa cha makolo anga.” Ndiyeno anakagona pabedi lake nʼkuyangʼana kukhoma ndipo anakana kudya.
-