1 Mafumu 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako mkazi wake Yezebeli+ anabwera nʼkumufunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani simukusangalala komanso mukukana kudya?”
5 Kenako mkazi wake Yezebeli+ anabwera nʼkumufunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani simukusangalala komanso mukukana kudya?”