1 Mafumu 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Yezebeli analemba makalata mʼdzina la Ahabu nʼkuwadinda ndi chidindo cha Ahabu.+ Kenako anatumiza makalatawo kwa akulu+ ndi anthu olemekezeka amumzinda umene Naboti ankakhala.
8 Choncho Yezebeli analemba makalata mʼdzina la Ahabu nʼkuwadinda ndi chidindo cha Ahabu.+ Kenako anatumiza makalatawo kwa akulu+ ndi anthu olemekezeka amumzinda umene Naboti ankakhala.