-
1 Mafumu 21:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Choncho amuna a mumzinda umene Naboti ankakhala, akulu ndi anthu olemekezeka amumzindawo, anachita mogwirizana ndi zimene zinali mʼmakalata amene Yezebeli anawatumizira.
-