1 Mafumu 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Ahabu anafunsa Eliya kuti: “Wandipeza kodi mdani wanga?”+ Eliya anayankha kuti: “Inde ndakupezani. Mulungu wanena kuti, ‘Chifukwa watsimikiza mtima kuti uchite zoipa pamaso pa Yehova,+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:20 Nsanja ya Olonda,2/1/2014, ptsa. 14-15
20 Ndiyeno Ahabu anafunsa Eliya kuti: “Wandipeza kodi mdani wanga?”+ Eliya anayankha kuti: “Inde ndakupezani. Mulungu wanena kuti, ‘Chifukwa watsimikiza mtima kuti uchite zoipa pamaso pa Yehova,+