1 Mafumu 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Komanso ponena za Yezebeli, Yehova wanena kuti, ‘Agalu adzamudya Yezebeli mʼmunda wa ku Yezereeli.+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:23 Yeremiya, tsa. 120
23 Komanso ponena za Yezebeli, Yehova wanena kuti, ‘Agalu adzamudya Yezebeli mʼmunda wa ku Yezereeli.+