-
1 Mafumu 21:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Ahabu atangomva mawu amenewa, anangʼamba zovala zake nʼkuvala chiguduli. Iye anayamba kusala kudya, kugona pachiguduli ndipo ankayenda mwachisoni.
-