1 Mafumu 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Kodi waona mmene Ahabu wadzichepetsera pamaso panga?+ Chifukwa wadzichepetsa pamaso panga, sindidzabweretsa tsokali iye adakali moyo. Mʼmalomwake, ndidzalibweretsa kwa anthu a mʼnyumba yake mʼnthawi ya mwana wake.”+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:29 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2021, tsa. 3 Nsanja ya Olonda,2/1/2014, tsa. 15
29 “Kodi waona mmene Ahabu wadzichepetsera pamaso panga?+ Chifukwa wadzichepetsa pamaso panga, sindidzabweretsa tsokali iye adakali moyo. Mʼmalomwake, ndidzalibweretsa kwa anthu a mʼnyumba yake mʼnthawi ya mwana wake.”+