1 Mafumu 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno mfumu ya Isiraeli inafunsa atumiki ake kuti: “Kodi mukudziwa kuti mzinda wa Ramoti-giliyadi+ ndi wathu? Koma tikuzengereza kuulanda mʼmanja mwa mfumu ya Siriya.”
3 Ndiyeno mfumu ya Isiraeli inafunsa atumiki ake kuti: “Kodi mukudziwa kuti mzinda wa Ramoti-giliyadi+ ndi wathu? Koma tikuzengereza kuulanda mʼmanja mwa mfumu ya Siriya.”