-
1 Mafumu 22:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Choncho mfumu ya Isiraeli inasonkhanitsa aneneri. Analipo amuna pafupifupi 400 ndipo inawafunsa kuti: “Kodi ndipite kukamenyana ndi Ramoti-giliyadi, kapena ndisapite?” Iwo anayankha kuti: “Pitani ndipo Yehova akapereka mzindawo kwa inu mfumu.”
-