1 Mafumu 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Yehosafati anati: “Kodi kuno kulibe mneneri wina wa Yehova? Ngati alipo, tiyeni tifunsirenso kwa Mulungu kudzera mwa iyeyo.”+
7 Kenako Yehosafati anati: “Kodi kuno kulibe mneneri wina wa Yehova? Ngati alipo, tiyeni tifunsirenso kwa Mulungu kudzera mwa iyeyo.”+