-
1 Mafumu 22:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ndiyeno Zedekiya mwana wa Kenaana anapanga nyanga zachitsulo nʼkunena kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Ndi nyanga izi mudzagunda Asiriya mpaka kuwapha onse.’”
-