-
1 Mafumu 22:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Kenako anafika kwa mfumu ndipo mfumuyo inamufunsa kuti: “Mikaya, kodi tipite kukamenyana ndi Ramoti-giliyadi kapena tisapite?” Nthawi yomweyo Mikaya anayankha kuti: “Pitani mukapambana ndipo Yehova akapereka mzindawo kwa inu mfumu.”
-