1 Mafumu 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho Mikaya anati: “Ndikuona Aisiraeli onse atabalalika mʼmapiri+ ngati nkhosa zopanda mʼbusa. Ndipo Yehova anati: ‘Amenewa alibe mtsogoleri. Aliyense abwerere kunyumba kwake mwamtendere.’”
17 Choncho Mikaya anati: “Ndikuona Aisiraeli onse atabalalika mʼmapiri+ ngati nkhosa zopanda mʼbusa. Ndipo Yehova anati: ‘Amenewa alibe mtsogoleri. Aliyense abwerere kunyumba kwake mwamtendere.’”