-
1 Mafumu 22:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ndiyeno Yehova anati, ‘Ndani akapusitse Ahabu, kuti apite ku Ramoti-giliyadi nʼkukafa?’ Choncho angelo osiyanasiyana ankanena maganizo awo, wina izi, wina izi.
-