1 Mafumu 22:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho Yehova waika mzimu wabodza mʼkamwa mwa aneneri anu onsewa,+ koma Yehovayo wanena kuti inuyo muona tsoka.”+
23 Choncho Yehova waika mzimu wabodza mʼkamwa mwa aneneri anu onsewa,+ koma Yehovayo wanena kuti inuyo muona tsoka.”+