1 Mafumu 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Zedekiya mwana wa Kenaana anapita pomwe panali Mikaya nʼkumumenya mbama ndipo ananena kuti: “Zingatheke bwanji kuti mzimu wa Yehova undidutse nʼkukalankhula ndi iwe?”+
24 Zedekiya mwana wa Kenaana anapita pomwe panali Mikaya nʼkumumenya mbama ndipo ananena kuti: “Zingatheke bwanji kuti mzimu wa Yehova undidutse nʼkukalankhula ndi iwe?”+