1 Mafumu 22:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Mfumu ya Siriya inali italamula akuluakulu 32 oyangʼanira asilikali okwera magaleta kuti:+ “Musakamenyane ndi wina aliyense, wamngʼono kapena wamkulu, koma mfumu ya Isiraeli yokha basi.”
31 Mfumu ya Siriya inali italamula akuluakulu 32 oyangʼanira asilikali okwera magaleta kuti:+ “Musakamenyane ndi wina aliyense, wamngʼono kapena wamkulu, koma mfumu ya Isiraeli yokha basi.”