1 Mafumu 22:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Nkhondoyo inafika poopsa tsiku limenelo ndipo mfumuyo anaiimiritsa mʼgaleta nʼkuitsamiritsa kugaletalo moyangʼanizana ndi Asiriya. Magazi ochokera pamene anaibaya paja ankayenderera mʼgaletamo ndipo kenako inafa madzulo.+
35 Nkhondoyo inafika poopsa tsiku limenelo ndipo mfumuyo anaiimiritsa mʼgaleta nʼkuitsamiritsa kugaletalo moyangʼanizana ndi Asiriya. Magazi ochokera pamene anaibaya paja ankayenderera mʼgaletamo ndipo kenako inafa madzulo.+