1 Mafumu 22:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Dzuwa litatsala pangʼono kulowa, mumsasamo analengeza kuti: “Aliyense azipita mumzinda wake ndi kudziko lake!”+
36 Dzuwa litatsala pangʼono kulowa, mumsasamo analengeza kuti: “Aliyense azipita mumzinda wake ndi kudziko lake!”+