1 Mafumu 22:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Atayamba kutsuka galeta lankhondolo padziwe la ku Samariya, lomwe mahule ankasambapo, agalu anayamba kunyambita magazi a mfumuyo mogwirizana ndi mawu amene Yehova ananena.+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:38 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo, Nsanja ya Olonda,2/1/2014, tsa. 15
38 Atayamba kutsuka galeta lankhondolo padziwe la ku Samariya, lomwe mahule ankasambapo, agalu anayamba kunyambita magazi a mfumuyo mogwirizana ndi mawu amene Yehova ananena.+