1 Mafumu 22:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Nkhani zina zokhudza Ahabu, zonse zimene anachita, nyumba yaminyanga ya njovu+ imene anamanga komanso mizinda yonse imene anamanga, zinalembedwa mʼbuku la mbiri ya mafumu a Isiraeli. 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:39 Nsanja ya Olonda,11/1/1990, ptsa. 16-17
39 Nkhani zina zokhudza Ahabu, zonse zimene anachita, nyumba yaminyanga ya njovu+ imene anamanga komanso mizinda yonse imene anamanga, zinalembedwa mʼbuku la mbiri ya mafumu a Isiraeli.