1 Mafumu 22:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Yehosafati+ mwana wa Asa anakhala mfumu ya Yuda mʼchaka cha 4 cha Ahabu mfumu ya Isiraeli.