-
1 Mafumu 22:42Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
42 Yehosafati anali ndi zaka 35 pamene ankakhala mfumu ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 25. Mayi ake dzina lawo linali Azuba mwana wa Sili.
-