1 Mafumu 22:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Yehosafati anachotsanso mʼdzikolo mahule aamuna apakachisi+ amene anatsala pa nthawi ya Asa bambo ake.+
46 Yehosafati anachotsanso mʼdzikolo mahule aamuna apakachisi+ amene anatsala pa nthawi ya Asa bambo ake.+