1 Mafumu 22:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Yehosafati anapanga zombo* za ku Tarisi kuti zizipita ku Ofiri kukatenga golide.+ Koma sizinapite chifukwa zinasweka ku Ezioni-geberi.+
48 Yehosafati anapanga zombo* za ku Tarisi kuti zizipita ku Ofiri kukatenga golide.+ Koma sizinapite chifukwa zinasweka ku Ezioni-geberi.+