-
1 Mafumu 22:49Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
49 Pa nthawi imeneyi mʼpamene Ahaziya mwana wa Ahabu anapempha Yehosafati kuti: “Bwanji antchito anga apite limodzi ndi antchito anu mʼzombozo?” Koma Yehosafati anakana.
-