1 Mafumu 22:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Kenako Yehosafati, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda a makolo ake+ mu Mzinda wa Davide kholo lake. Ndiyeno mwana wake Yehoramu+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.
50 Kenako Yehosafati, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda a makolo ake+ mu Mzinda wa Davide kholo lake. Ndiyeno mwana wake Yehoramu+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.