1 Mafumu 22:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Ahaziya anapitiriza kutumikira Baala+ komanso kumugwadira. Anapitiriza kukwiyitsa Yehova Mulungu wa Isiraeli+ ngati mmene anachitira bambo ake.
53 Ahaziya anapitiriza kutumikira Baala+ komanso kumugwadira. Anapitiriza kukwiyitsa Yehova Mulungu wa Isiraeli+ ngati mmene anachitira bambo ake.