2 Mafumu 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Komanso iwo ankawotcha* pamoto ana awo aamuna ndi aakazi,+ kulosera+ ndiponso kuwombeza. Anatsimikiza mtima kuchita zoipa pamaso pa Yehova nʼcholinga chomukwiyitsa.
17 Komanso iwo ankawotcha* pamoto ana awo aamuna ndi aakazi,+ kulosera+ ndiponso kuwombeza. Anatsimikiza mtima kuchita zoipa pamaso pa Yehova nʼcholinga chomukwiyitsa.