-
2 Mafumu 17:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Yehova anakana anthu onse omwe anali mbadwa za Isiraeli ndipo anawachititsa manyazi nʼkuwapereka mʼmanja mwa anthu omwe anawalanda katundu, mpaka iye anawachotsa pamaso pake.
-