2 Mafumu 17:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anangʼamba Isiraeli kumusiyanitsa ndi nyumba ya Davide ndipo iwo anaveka ufumu Yerobowamu mwana wa Nebati.+ Yerobowamuyo anasocheretsa Aisiraeli kuti asiye kutsatira Yehova nʼkuwachititsa tchimo lalikulu.
21 Anangʼamba Isiraeli kumusiyanitsa ndi nyumba ya Davide ndipo iwo anaveka ufumu Yerobowamu mwana wa Nebati.+ Yerobowamuyo anasocheretsa Aisiraeli kuti asiye kutsatira Yehova nʼkuwachititsa tchimo lalikulu.