2 Mafumu 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 mpaka Yehova anachotsa Aisiraeli pamaso pake ngati mmene ananenera kudzera mwa atumiki ake onse, aneneri.+ Choncho Aisiraeli anatengedwa mʼdziko lawo nʼkupita nawo ku Asuri+ ndipo ali komweko mpaka lero.
23 mpaka Yehova anachotsa Aisiraeli pamaso pake ngati mmene ananenera kudzera mwa atumiki ake onse, aneneri.+ Choncho Aisiraeli anatengedwa mʼdziko lawo nʼkupita nawo ku Asuri+ ndipo ali komweko mpaka lero.