2 Mafumu 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako mfumu ya Asuri inatenga anthu kuchokera ku Babulo, ku Kuta, ku Ava, ku Hamati ndi ku Sefaravaimu+ nʼkuwaika mʼmizinda ya ku Samariya mʼmalo mwa Aisiraeli. Anthuwo anatenga Samariya nʼkumakhala mʼmizinda yake. 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:24 Nsanja ya Olonda,2/15/1988, tsa. 27
24 Kenako mfumu ya Asuri inatenga anthu kuchokera ku Babulo, ku Kuta, ku Ava, ku Hamati ndi ku Sefaravaimu+ nʼkuwaika mʼmizinda ya ku Samariya mʼmalo mwa Aisiraeli. Anthuwo anatenga Samariya nʼkumakhala mʼmizinda yake.