2 Mafumu 17:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Atayamba kukhala kumeneko, sankaopa* Yehova. Choncho Yehova anawatumizira mikango+ ndipo inapha ena mwa anthuwo.
25 Atayamba kukhala kumeneko, sankaopa* Yehova. Choncho Yehova anawatumizira mikango+ ndipo inapha ena mwa anthuwo.